1 Mbiri 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Uza ndipo anamupha chifukwa anatambasula dzanja lake nʼkugwira Likasa,+ moti Uza anafera pomwepo pamaso pa Mulungu.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:10 Nsanja ya Olonda,2/1/2005, ptsa. 26-27
10 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Uza ndipo anamupha chifukwa anatambasula dzanja lake nʼkugwira Likasa,+ moti Uza anafera pomwepo pamaso pa Mulungu.+