1 Mbiri 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Afilisiti atamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Aisiraeli onse,+ Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide.+ Davide atamva zimenezi, anapita kukamenyana nawo.
8 Afilisiti atamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Aisiraeli onse,+ Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide.+ Davide atamva zimenezi, anapita kukamenyana nawo.