1 Mbiri 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa chakuti ulendo woyamba uja si inuyo amene munalinyamula,+ Yehova Mulungu wathu anatikwiyira koopsa,+ popeza sitinatsatire malangizo ake.”+
13 Chifukwa chakuti ulendo woyamba uja si inuyo amene munalinyamula,+ Yehova Mulungu wathu anatikwiyira koopsa,+ popeza sitinatsatire malangizo ake.”+