-
1 Mbiri 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Komanso anapatsa Aisiraeli onse mikate yozungulira, makeke a zipatso za kanjedza ndi makeke a mphesa. Anapereka zimenezi kwa aliyense, mwamuna ndiponso mkazi.
-