1 Mbiri 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye ndi Yehova Mulungu wathu.+ Ziweruzo zake zili padziko lonse lapansi.+