1 Mbiri 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mulungu sanalole kuti munthu aliyense awapondereze,+Koma anadzudzula mafumu chifukwa cha iwo.+