1 Mbiri 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kumwamba kukondwere ndipo dziko lapansi lisangalale,+Lengezani kwa anthu a mitundu ina kuti: ‘Yehova wakhala Mfumu!’+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:31 Nsanja ya Olonda,1/15/2014, ptsa. 10-11
31 Kumwamba kukondwere ndipo dziko lapansi lisangalale,+Lengezani kwa anthu a mitundu ina kuti: ‘Yehova wakhala Mfumu!’+