-
1 Mbiri 17:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pa nthawi yonse imene ndinkayenda ndi Aisiraeli, kodi ndinayamba ndafunsapo oweruza a Isiraeli amene ndinawasankha kuti azitsogolera anthu anga kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani simunandimangire nyumba ya mitengo ya mkungudza?’”’
-