1 Mbiri 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Mfumu Davide anakhala pansi pamaso pa Yehova ndipo anati: “Ndine ndani ine, inu Yehova Mulungu? Ndipo banja lathu* nʼchiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano?+
16 Kenako Mfumu Davide anakhala pansi pamaso pa Yehova ndipo anati: “Ndine ndani ine, inu Yehova Mulungu? Ndipo banja lathu* nʼchiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano?+