1 Mbiri 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, palibe amene angafanane ndi inu+ komanso palibe Mulungu wina koma inu nokha.+ Zonse zimene tamva zikutsimikizira zimenezi.
20 Inu Yehova, palibe amene angafanane ndi inu+ komanso palibe Mulungu wina koma inu nokha.+ Zonse zimene tamva zikutsimikizira zimenezi.