-
1 Mbiri 17:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndi mtundu uti padziko lapansi umene ungafanane ndi mtundu wa anthu anu Aisiraeli?+ Inu Mulungu woona munapita kukawombola anthu anu.+ Komanso munadzipangira dzina pamene munawachitira zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha,+ pothamangitsa mitundu ina pamaso pa anthu anu+ amene munawawombola ku Iguputo.
-