1 Mbiri 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munachititsa Aisiraeli kuti akhale anthu anu nthawi zonse.+ Ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wawo.+
22 Munachititsa Aisiraeli kuti akhale anthu anu nthawi zonse.+ Ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wawo.+