1 Mbiri 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho inu Yehova, chitani zimene mwalonjeza zokhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake ndipo muchite zimenezi mpaka kalekale. Muchite mogwirizana ndi zimene mwalonjeza.+
23 Choncho inu Yehova, chitani zimene mwalonjeza zokhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake ndipo muchite zimenezi mpaka kalekale. Muchite mogwirizana ndi zimene mwalonjeza.+