1 Mbiri 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa inu, Mulungu wanga, mwandiululira ine mtumiki wanu cholinga chanu choti mukufuna kundimangira nyumba.* Nʼchifukwa chake ine mtumiki wanu ndalimba mtima kupemphera kwa inu pempheroli.
25 Chifukwa inu, Mulungu wanga, mwandiululira ine mtumiki wanu cholinga chanu choti mukufuna kundimangira nyumba.* Nʼchifukwa chake ine mtumiki wanu ndalimba mtima kupemphera kwa inu pempheroli.