-
1 Mbiri 17:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho dalitsani nyumba ya ine mtumiki wanu kuti ikhazikike pamaso panu mpaka kalekale. Chifukwa inu Yehova mwadalitsa nyumba ya ine mtumiki wanu ndipo yadalitsika mpaka kalekale.”
-