1 Mbiri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anagonjetsa Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ pafupi ndi Hamati,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kukakhazikitsa ulamuliro wake kumtsinje wa Firate.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:3 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 11
3 Davide anagonjetsa Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ pafupi ndi Hamati,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kukakhazikitsa ulamuliro wake kumtsinje wa Firate.+