1 Mbiri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako panayambikanso nkhondo ina ku Gati+ ndipo kunali munthu wamkulu modabwitsa.+ Iye anali ndi zala 6 kudzanja lililonse ndiponso zala 6 kuphazi lililonse, moti anali ndi zala 24. Nayenso anali mbadwa ya Arefai.+
6 Kenako panayambikanso nkhondo ina ku Gati+ ndipo kunali munthu wamkulu modabwitsa.+ Iye anali ndi zala 6 kudzanja lililonse ndiponso zala 6 kuphazi lililonse, moti anali ndi zala 24. Nayenso anali mbadwa ya Arefai.+