-
1 Mbiri 21:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Zaka zitatu za njala+ kapena miyezi itatu yoti adani anu akuseseni ndi kukuphani ndi lupanga lawo,+ kapenanso masiku atatu a lupanga la Yehova, lomwe ndi mliri umene udzagwe mʼdziko+ lanu pamene mngelo wa Yehova adzawononge+ madera onse a Isiraeli.’ Ganizirani zoti ndikayankhe kwa amene wandituma.”
-