1 Mbiri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Undigulitse* malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe kuti mliriwu uthe pakati pa anthuwa.+ Undiuze ndalama zake zonse.”
22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Undigulitse* malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe kuti mliriwu uthe pakati pa anthuwa.+ Undiuze ndalama zake zonse.”