1 Mbiri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mfumu Davide inauza Orinani kuti: “Ayi, ndikuyenera kugula ndipo ndipereka ndalama zake zonse, chifukwa sindingatenge zinthu zako nʼkupereka kwa Yehova kapena kupereka nsembe zopsereza popanda kulipira chilichonse.”+
24 Koma Mfumu Davide inauza Orinani kuti: “Ayi, ndikuyenera kugula ndipo ndipereka ndalama zake zonse, chifukwa sindingatenge zinthu zako nʼkupereka kwa Yehova kapena kupereka nsembe zopsereza popanda kulipira chilichonse.”+