1 Mbiri 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, Davide analamula kuti asonkhanitse alendo okhala mʼdziko la Isiraeli.+ Alendowo anawapatsa ntchito yosema miyala, kuti azisema miyala yomangira nyumba ya Mulungu woona.+
2 Atatero, Davide analamula kuti asonkhanitse alendo okhala mʼdziko la Isiraeli.+ Alendowo anawapatsa ntchito yosema miyala, kuti azisema miyala yomangira nyumba ya Mulungu woona.+