-
1 Mbiri 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Davide anati: “Mwana wanga Solomo ndi wamngʼono komanso sadziwa zambiri+ ndipo nyumba yoti adzamangire Yehova idzakhala yaikulu, yokongola+ ndi yogometsa+ nʼcholinga choti idzakhale yodziwika padziko lonse.+ Ndiye ndimukonzera zipangizo zoti adzagwiritsire ntchito.” Choncho Davide asanafe, anasonkhanitsa zipangizo zambirimbiri pokonzekera ntchitoyo.
-