1 Mbiri 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Simeyi anali Yahati, Zina,* Yeusi ndi Beriya. Ana 4 amenewa anali a Simeyi.