1 Mbiri 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mbadwa* za Eliezere, mtsogoleri wawo anali Rehabiya.+ Eliezere sanakhalenso ndi ana ena aamuna, koma Rehabiya anali ndi ana aamuna ambirimbiri.
17 Mbadwa* za Eliezere, mtsogoleri wawo anali Rehabiya.+ Eliezere sanakhalenso ndi ana ena aamuna, koma Rehabiya anali ndi ana aamuna ambirimbiri.