1 Mbiri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Heburoni anali Yeriya, amene anali mtsogoleri wawo, wachiwiri wake anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli ndipo wa 4 anali Yekameamu.+
19 Ana a Heburoni anali Yeriya, amene anali mtsogoleri wawo, wachiwiri wake anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli ndipo wa 4 anali Yekameamu.+