1 Mbiri 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana a Uziyeli+ anali Mika, amene anali mtsogoleri wawo ndipo Isiya anali wachiwiri wake.