-
1 Mbiri 24:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Semaya mwana wa Netaneli mlembi wa Alevi, anawalemba mayina pamaso pa mfumu, akalonga, wansembe Zadoki,+ Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara+ ndiponso pamaso pa atsogoleri a nyumba za makolo za ansembe ndi za Alevi. Ankasankha nyumba imodzi ya makolo kuchokera kwa ana a Eleazara kenako nʼkusankhanso nyumba imodzi ya makolo kuchokera kwa ana a Itamara.
-