1 Mbiri 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene ankachitira utumiki wawo+ akalowa mʼnyumba ya Yehova mogwirizana ndi dongosolo limene Aroni kholo lawo anakhazikitsa ngati mmene Yehova Mulungu wa Isiraeli anamulamulira.
19 Umu ndi mmene ankachitira utumiki wawo+ akalowa mʼnyumba ya Yehova mogwirizana ndi dongosolo limene Aroni kholo lawo anakhazikitsa ngati mmene Yehova Mulungu wa Isiraeli anamulamulira.