-
1 Mbiri 26:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Onsewa anali mbadwa za Obedi-edomu. Iwowa, ana awo ndi abale awo anali odalirika ndi oyenerera kutumikira. Onse analipo 62 ndipo anali mbadwa za Obedi-edomu.
-