1 Mbiri 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kumbali ya mbadwa za Heburoni,+ panali Hasabiya ndi abale ake, amuna odalirika okwana 1,700. Iwowa ankayangʼanira Aisiraeli mʼchigawo chakumadzulo kwa Yorodano pa ntchito zonse za Yehova ndiponso zotumikira mfumu.
30 Kumbali ya mbadwa za Heburoni,+ panali Hasabiya ndi abale ake, amuna odalirika okwana 1,700. Iwowa ankayangʼanira Aisiraeli mʼchigawo chakumadzulo kwa Yorodano pa ntchito zonse za Yehova ndiponso zotumikira mfumu.