-
1 Mbiri 26:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ndipo abale a Yereya, amuna odalirika komanso atsogoleri a nyumba za makolo awo, analipo 2,700. Choncho Mfumu Davide inawaika kuti aziyangʼanira anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase pa nkhani iliyonse yokhudza Mulungu woona ndiponso yokhudza mfumu.
-