-
1 Mbiri 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Benaya ameneyu anali mwamuna wamphamvu pa amuna 30 komanso anali mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Pagulu lakelo, mwana wake Amizabadi ndi amene anali mtsogoleri.
-