1 Mbiri 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Azimaveti mwana wa Adieli ankayangʼanira chuma cha mfumu.+ Yonatani mwana wa Uziya ankayangʼanira mosungira katundu mʼmadera apafupi, mʼmizinda, mʼmidzi ndi munsanja zosiyanasiyana.
25 Azimaveti mwana wa Adieli ankayangʼanira chuma cha mfumu.+ Yonatani mwana wa Uziya ankayangʼanira mosungira katundu mʼmadera apafupi, mʼmizinda, mʼmidzi ndi munsanja zosiyanasiyana.