1 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mfumu Davide anauza mpingo wonse kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamngʼono ndipo sadziwa zambiri.+ Ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa si kachisi* wa munthu koma wa Yehova Mulungu.+
29 Mfumu Davide anauza mpingo wonse kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamngʼono ndipo sadziwa zambiri.+ Ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa si kachisi* wa munthu koma wa Yehova Mulungu.+