1 Mbiri 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso chifukwa chakuti ndikusangalala ndi nyumba ya Mulungu wanga,+ kuwonjezera pa zonse zimene ndakonzekera zokhudza nyumba yopatulikayo, ndikupereka kunyumba ya Mulungu wanga chuma changa+ chomwe ndi golide ndi siliva.
3 Komanso chifukwa chakuti ndikusangalala ndi nyumba ya Mulungu wanga,+ kuwonjezera pa zonse zimene ndakonzekera zokhudza nyumba yopatulikayo, ndikupereka kunyumba ya Mulungu wanga chuma changa+ chomwe ndi golide ndi siliva.