-
1 Mbiri 29:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Inu Yehova Mulungu wathu, chuma chonse chimene takonzekera kuti tikumangireni nyumba ya dzina lanu loyera nʼchochokera mʼdzanja lanu ndipo zonse ndi zanu.
-