1 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsikulo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri+ pamaso pa Yehova. Kachiwirinso, anaveka Solomo mwana wa Davide ufumu ndipo anamudzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki kukhala wansembe.+
22 Pa tsikulo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri+ pamaso pa Yehova. Kachiwirinso, anaveka Solomo mwana wa Davide ufumu ndipo anamudzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki kukhala wansembe.+