2 Mbiri 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano inu Yehova Mulungu, kwaniritsani lonjezo limene munapereka kwa Davide bambo anga+ popeza mwandiika kukhala mfumu ya anthuwa, omwe ndi ochuluka kwambiri ngati fumbi.+
9 Tsopano inu Yehova Mulungu, kwaniritsani lonjezo limene munapereka kwa Davide bambo anga+ popeza mwandiika kukhala mfumu ya anthuwa, omwe ndi ochuluka kwambiri ngati fumbi.+