2 Mbiri 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ndani angathe kumangira Mulunguyo nyumba? Chifukwa kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, nʼkosakwanira kuti akhaleko.+ Ndiye ine ndine ndani kuti ndimumangire nyumba, kupatulapo yoperekeramo nsembe pamaso pake?
6 Ndipo ndani angathe kumangira Mulunguyo nyumba? Chifukwa kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, nʼkosakwanira kuti akhaleko.+ Ndiye ine ndine ndani kuti ndimumangire nyumba, kupatulapo yoperekeramo nsembe pamaso pake?