2 Mbiri 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide+ bambo ake. Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza, pamalo opunthira mbewu a Orinani+ Muyebusi.
3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide+ bambo ake. Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza, pamalo opunthira mbewu a Orinani+ Muyebusi.