2 Mbiri 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mapiko a akerubiwo+ anali aatali mikono 20. Phiko limodzi la kerubi woyamba linali lalitali mikono 5 ndipo linagunda khoma la chipindacho. Phiko lina linalinso lalitali mikono 5 ndipo linakagunda phiko la kerubi wina.
11 Mapiko a akerubiwo+ anali aatali mikono 20. Phiko limodzi la kerubi woyamba linali lalitali mikono 5 ndipo linagunda khoma la chipindacho. Phiko lina linalinso lalitali mikono 5 ndipo linakagunda phiko la kerubi wina.