-
2 Mbiri 6:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma Yehova anauza Davide bambo anga kuti, ‘Unkafunitsitsa kumanga nyumba ya dzina langa ndipo unachita bwino kulakalaka utachita zimenezi.
-