13 (Solomo anapanga nsanja yakopa nʼkuiika pakati pa bwalo lamkati.+ Nsanjayo inali yaikulu mikono 5 mulitali, mikono 5 mulifupi ndiponso mikono itatu kupita mʼmwamba. Iye anakwera pansanjayo.) Ndiyeno anagwada patsogolo pa Aisiraeli onse nʼkukweza manja ake mʼmwamba.+