2 Mbiri 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero anati: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli, palibe Mulungu wina wofanana ndi inu kumwambako kapena pansi pano. Mumasunga pangano komanso mumasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amakutumikirani ndi mtima wawo wonse.+
14 Atatero anati: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli, palibe Mulungu wina wofanana ndi inu kumwambako kapena pansi pano. Mumasunga pangano komanso mumasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amakutumikirani ndi mtima wawo wonse.+