2 Mbiri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma kodi Mulungu angakhaledi limodzi ndi anthu padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+
18 Koma kodi Mulungu angakhaledi limodzi ndi anthu padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+