-
2 Mbiri 6:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Inu Yehova Mulungu wanga, mumvetsere pemphero la mtumiki wanu ndi pempho lake lopempha chifundo. Imvani kulira kwanga kopempha thandizo komanso pemphero limene ine mtumiki wanu ndikupemphera kwa inu.
-