2 Mbiri 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu anu Aisiraeli akagonjetsedwa ndi adani awo chifukwa choti ankakuchimwirani,+ ndiyeno abwerera kwa inu nʼkutamanda dzina lanu+ mʼnyumbayi, kupemphera+ ndiponso kupempha kuti muwachitire chifundo,+
24 Anthu anu Aisiraeli akagonjetsedwa ndi adani awo chifukwa choti ankakuchimwirani,+ ndiyeno abwerera kwa inu nʼkutamanda dzina lanu+ mʼnyumbayi, kupemphera+ ndiponso kupempha kuti muwachitire chifundo,+