2 Mbiri 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 inuyo mumve muli kumwambako ndipo anthu anu Aisiraeli, omwenso ndi atumiki anu, muwakhululukire machimo awo popeza mudzawaphunzitsa njira yabwino yoti aziyendamo.+ Mubweretse mvula+ mʼdziko lanu limene munapatsa anthu anu monga cholowa.
27 inuyo mumve muli kumwambako ndipo anthu anu Aisiraeli, omwenso ndi atumiki anu, muwakhululukire machimo awo popeza mudzawaphunzitsa njira yabwino yoti aziyendamo.+ Mubweretse mvula+ mʼdziko lanu limene munapatsa anthu anu monga cholowa.