2 Mbiri 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ndiyeno munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli akapereka pemphero lililonse,+ akapempha kuti muwachitire chifundo+ (chifukwa aliyense akudziwa mliri wake ndi ululu wake),+ ndiponso akakweza manja awo atayangʼana kunyumbayi,+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:29 Nsanja ya Olonda,12/1/2010, tsa. 113/15/2008, ptsa. 12-131/1/2004, tsa. 324/15/1997, tsa. 4
29 ndiyeno munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli akapereka pemphero lililonse,+ akapempha kuti muwachitire chifundo+ (chifukwa aliyense akudziwa mliri wake ndi ululu wake),+ ndiponso akakweza manja awo atayangʼana kunyumbayi,+