2 Mbiri 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 inuyo mumve muli kumwambako, komwe mumakhala+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu. Mupereke mphoto kwa aliyense mogwirizana ndi njira zake zonse, chifukwa mukudziwa mtima wake (inu nokha mumadziwa bwino mtima wa munthu aliyense).+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:30 Nsanja ya Olonda,12/1/2010, tsa. 113/15/2008, ptsa. 12-131/1/2004, tsa. 32
30 inuyo mumve muli kumwambako, komwe mumakhala+ ndipo mukhululuke+ ndi kuchitapo kanthu. Mupereke mphoto kwa aliyense mogwirizana ndi njira zake zonse, chifukwa mukudziwa mtima wake (inu nokha mumadziwa bwino mtima wa munthu aliyense).+